CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Kodi Yehova Amafuna Kuti Tizimulambila Motani?
Aisiraeli anayenela kumvela Yehova, kum’konda na kum’tumikila na mtima wawo wonse komanso moyo wawo wonse (Deut. 11:13; it-2 1007 ¶4)
Ciliconse cokhudzana na kulambila konama cinayenela kuwonongedwa kothelatu (Deut. 12:2, 3)
Onse anafunika kulambila Mulungu pa malo amodzi (Deut. 12:11-14; it-1 84 ¶3)
Yehova amafuna kuti anthu ake azimulambila na moyo wawo wonse, azipewa kulambila konama kwa mtundu uliwonse, komanso kuti azikhala ogwilizana.