LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 July tsa. 7
  • Moyo wa Munthu Ni Wamtengo Wapatali Kwa Yehova

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Moyo wa Munthu Ni Wamtengo Wapatali Kwa Yehova
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • Thaŵilani kwa Yehova
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nyamulani Mwana Wanu
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Kodi Mukumbukila?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2017
  • Kodi Yehova Amafuna Kuti Tizimulambila Motani?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 July tsa. 7

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Moyo wa Munthu Ni Wamtengo Wapatali Kwa Yehova

Mizinda yothaŵilako inali yosavuta munthu kufikako (Deut. 19:2, 3; w17.11 14 ¶4)

Mizinda yothaŵilako inali kuteteza Aisiraeli ku mlandu wa magazi (Deut. 19:10; w17.11 15 ¶9)

Kuzonda m’bale wathu kungatigwetsele mu mlandu wa magazi (Deut. 19:11-13; it-1 344)

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ningaonetse m’njila ziti kuti nimaona moyo mmene Yehova amauonela?’

Zithunzi: 1. M’bale alemba meseji pamene ayendetsa motoka. 2. M’bale mmodzi-modziyo akulemba meseji ataimilila pafupi na motoka yake imene waimika.
    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani