LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 May tsa. 6
  • Thaŵilani kwa Yehova

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Thaŵilani kwa Yehova
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • Moyo wa Munthu Ni Wamtengo Wapatali Kwa Yehova
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Kodi Mumathaŵila kwa Yehova?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2017
  • Nyamulani Mwana Wanu
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Kodi Mukumbukila?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2017
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 May tsa. 6

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Thaŵilani kwa Yehova

Mu Isiraeli, munali mizinda 6 imene aliyense wopha munthu mwangozi anali kuthaŵilako (Num. 35:15; w17.11 9 ¶4)

Mu Isiraeli, akulu ndiwo anali kuweluza mlandu wopha munthu (Num. 35:24; w17.11 9 ¶6)

Mizinda yothaŵilako inali kuteteza anthu amene apha munthu mwangozi (Num. 35:25; w17.11 11 ¶13)

Munthu wopha mnzake mwangozi anafunika kudzimana zinazake kuti akhale na mwayi wotetezeka mumzinda wothaŵilako. Nafenso tiyenela kudzimana zinthu zina kuti Yehova aticitile cifundo na kutikhululukila.

Mnyamata wagwetsa nkhope moonetsa kuvutika mtima. Zithunzi: Kufuna-funa cikhululukilo ca Yehova. 1. Munthu wocimwa amene walapa m’nthawi ya Aisiraeli akufotokoza mlandu wake kwa akulu pa cipata ca mzinda. 2. Mnyamata wolapa uja wapita kukaonana na akulu aŵili.
    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani