LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 July tsa. 4
  • Mmene Cilamulo Cinaonetsela Kuti Yehova Amadela Nkhawa Osauka

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Mmene Cilamulo Cinaonetsela Kuti Yehova Amadela Nkhawa Osauka
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • Mfundo Zothandiza Kuweluza Milandu Mwacilungamo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Utumiki wa Alevi
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Kodi Yehova Amafuna Kuti Tizimulambila Motani?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Kusamvela Malamulo a Mulungu Kumabweletsa Mavuto
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 July tsa. 4
Zithunzi: 1. Mwisiraeli amasula kapolo wake waciheberi. 2. Munthu apatsa mnzake mpukutu womata.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Mmene Cilamulo Cinaonetsela Kuti Yehova Amadela Nkhawa Osauka

Anthu osauka komanso anthu amene analibe coloŵa anali kuthandizidwa na mtundu wa Isiraeli (Deut. 14:28, 29; it-2 1110 ¶3)

M’caka ca Sabata, Aisiraeli amene anali na nkhongole anali ‘kumasulidwa’ ku nkhongole zawo (Deut. 15:1-3; it-2 833)

M’caka ca 7 pa zaka zimene wagwila nchito, Mwisiraeli amene anadzigulitsa kukhala kapolo anali kumasulidwa, ndipo mbuye wake anali kum’patsa mphatso (Deut. 15:12-14; it-2 978 6)

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi Akhristu osoŵa ningawaonetse cifundo m’njila ziti?’

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani