LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 January tsa. 14
  • Utumiki wa Alevi

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Utumiki wa Alevi
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • Kulambila pa Kacisi Kunayamba Kucitika Mwadongosolo Kwambili
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Mmene Cilamulo Cinaonetsela Kuti Yehova Amadela Nkhawa Osauka
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • “Ine Ndine . . . Colowa Cako”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Zimene Tingaphunzile pa Dongosolo la Msasa wa Aisiraeli
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 January tsa. 14
Zithunzi: Alevi akugwila nchito zosiyana-siyana. 1. Mlevi akuthila madzi m’beseni lamkuwa. 2. Mlevi akuguza ngolo yodzala na mitsuko. 3. Mlevi wanyamula mtsuko paphewa.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Utumiki wa Alevi

Yehova anatenga Alevi m’malo mwa ana aamuna oyamba kubadwa a Aisiraeli (Num. 3:11-13; it-2 683 ¶3)

Alevi anali kucita utumiki wapadela kwambili (Num. 3:25, 26, 31, 36, 37; it-2 241)

Alevi a zaka za pakati pa 30 mpaka 50 anali kucita nchito zawo zonse (Num. 4:46-48; it-2 241)

Amuna a m’banja la Aroni akugwila nchito za unsembe. Alevi ena onse akuwathandiza. Ni mmenenso zilili mumpingo wacikhristu masiku ano. Abale ena amasamalila maudindo akulu-akulu, pamene ena amasamalila nchito zina zofunikila za masiku onse.

M’bale wacinyamata akuyang’ana mosamala fomu ya mpingo yoodelapo mabuku. M’bale wacikulile akumuyang’ana uku akumwetulila.
    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani