LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 March tsa. 2
  • Zimene Tingaphunzile pa Dongosolo la Msasa wa Aisiraeli

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Zimene Tingaphunzile pa Dongosolo la Msasa wa Aisiraeli
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • Mmene Yehova Amatsogolela Anthu Ake
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Yehova Anawamenyela Nkhondo Aisiraeli
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Muzikwanilitsa Malumbilo Anu
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Utumiki wa Alevi
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 March tsa. 2

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Zimene Tingaphunzile pa Dongosolo la Msasa wa Aisiraeli

Amuna a paudindo amapeleka citsanzo cabwino pa utumiki wopatulika (Num. 7:10; it-1 497 ¶3)

Atumiki a Mulungu ayenela kukhala olinganizidwa bwino komanso adongosolo (Num. 7:11; it-2 796 ¶1)

Yehova amadziŵa bwino zimene aliyense wa ife sangakwanitse kucita (Num. 8:25, 26; w04 8/1 25 ¶1)

Monga mmene Yehova analinganizila Aisiraeli monga gulu, walinganizanso anthu ake monga gulu masiku ano. Ngakhale n’conco, iye amatiŵelengela aliyense payekha, ndipo amaona khama lathu pom’tumikila.

Zithunzi: Amuna apaudindo akutsogolela pa nchito za mpingo. 1. Mkulu na m’bale wacinyamata akuyeletsa mipando m’Nyumba ya Ufumu. 2. Mkulu akutsogolela kagulu mu ulaliki wa ku nyumba na nyumba. 3. Mkulu akupemphela pa miting’i ya akulu.
    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani