LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 March tsa. 12
  • April 19-25

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • April 19-25
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 March tsa. 12

April 19-25

NUMERI 22-24

  • Nyimbo 8 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yehova Anasintha Tembelelo Kukhala Dalitso”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu (Mph. 10)

    • Num. 22:20-22—Kodi n’cifukwa ciani Yehova anamukwiila Balamu? (w04 8/1 27 ¶2)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Num. 23:11-26 (th phunzilo 2)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • “Wonjezelani Cimwemwe Canu mu Ulaliki​—Seŵenzetsani Mawu a Mulungu”: (Mph. 10) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Pezani Cimwemwe pa Nchito Yopanga Ophunzila—Nolani Maluso Anu—Lolani Mphamvu ya Mawu a Mulungu Kugwila Nchito.

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) fg phunzilo 5 ¶3-4 (th phunzilo 6)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 38

  • “Yehova Asintha Cizunzo Kukhala Njila Yocitila Umboni”: (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Kufunsa Mafunso M’bale Dmitriy Mikhaylov.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30.) lfb phunzilo 32, 33

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 33 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani