LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 March tsa. 8
  • March 29–April 4

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • March 29–April 4
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 March tsa. 8

March 29–April 4

NUMERI 15-16

  • Nyimbo 101 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Samalani na Kunyada Komanso Kudzidalila”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Num. 15:32-35—Kodi tiphunzilapo ciani pa nkhani imeneyi? (w98 9/1 20 ¶1-2)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Num. 15:1-16 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Woyamba: Yesu—Mat. 16:16. Nthawi iliyonse vidiyo ikaima, na imwe iimitseni na kufunsa omvetsela mafunso amene aonekela pa sikilini.

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 1)

  • Nkhani: (Mph. 5) w15 5/15 15 ¶5-6—Mutu: Kodi Kunyadila na Kunyada N’zosiyana Bwanji? (th phunzilo 8)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 124

  • “Pewani Kutengela Anthu Osakhulupilika”: (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Pewani Kutengela Anthu Osakhulupilika.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 29

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 97 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani