LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 March tsa. 14
  • April 26–May 2

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • April 26–May 2
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 March tsa. 14

April 26–May 2

NUMERI 25–26

  • Nyimbo 135 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kodi Zocita za Munthu Mmodzi Zingapindulitse Ambili?”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu (Mph. 10)

    • Num. 26:55, 56—Kodi Yehova anaonetsa bwanji nzelu pogaŵa malo a colowa kwa mafuko a Aisiraeli? (it-1 359 ¶1-2)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Num. 25:1-18 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Seŵenzetsani Makambilano Acitsanzo. (th phunzilo 1)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo. Chulani na kukambilana vidiyo imene mwasankha (koma musaitambitse). (th phunzilo 3)

  • Nkhani: (Mph. 5) w04 4/1 29—Mutu: N’cifukwa ciani ciŵelengelo ca anthu cochulidwa pa Numeri 25:9 n’cosiyana na ca pa 1 Akorinto 10:8? (th phunzilo 17)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 28

  • “Sankhani Mabwenzi Mwanzelu”: (Mph 15) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Zitsanzo Zoticenjeza Masiku Ano—Kambali Kake. Limbikitsani onse kuti akaonelele vidiyo yonse.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 34

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 126 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani