LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 March tsa. 14
  • Kodi Zocita za Munthu Mmodzi Zingapindulitse Ambili?

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kodi Zocita za Munthu Mmodzi Zingapindulitse Ambili?
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • Mmene Yehova Amatsogolela Anthu Ake
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • “Ine Ndine . . . Colowa Cako”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Yehova Anasintha Tembelelo Kukhala Dalitso
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Mmene Cikhulupililo Cimatithandizila Kukhala Olimba Mtima
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 March tsa. 14

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kodi Zocita za Munthu Mmodzi Zingapindulitse Ambili?

Amoabu ananyengelela Aisiraeli kucita zoipa (Num. 25:1, 2; lvs 118 ¶1-2)

Mkwiyo wa Yehova unayakila Aisiraeli cifukwa ca kusakhulupilika na kudzikonda kwawo (Num. 25:3-5; lvs 119 ¶4)

Mkwiyo wa Yehova unatha pamene munthu mmodzi anacitapo kanthu molimba mtima (Num. 25:6-11)

Mlongo wacitsikana akuseŵenzetsa bulosha yakuti ‘Mmene Moyo Unayambila’ popeleka lipoti kwa anzake m’kilasi. Mwana wa sukulu mmodzi wakweza dzanja.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Ni pa zocitika ziti pamene niyenela kulimba mtima kuti nikhale wosiyana na ena?’

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani