LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 March tsa. 12
  • Yehova Anasintha Tembelelo Kukhala Dalitso

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yehova Anasintha Tembelelo Kukhala Dalitso
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • Utumiki wa Alevi
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Zimene Tingaphunzile pa Dongosolo la Msasa wa Aisiraeli
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Mmene Yehova Amatsogolela Anthu Ake
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • N’cifukwa Ciani Tiyenela Kupewa Mzimu Wodandaula?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 March tsa. 12
Alongo aŵili akulalikila mayi amene akucotsa zinyalala panyumba pambuyo pa ngozi ya zacilengedwe.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yehova Anasintha Tembelelo Kukhala Dalitso

Amoabu anafuna kutembelela Aisiraeli (Num. 22:3-6)

Yehova anateteza anthu ake (Num. 22:12, 34, 35; 23:11, 12)

Palibe angapambane polimbana na Yehova (Num. 24:12, 13; bt 53 ¶5; it-2 291)

Palibe cimene cingalepheletse uthenga wabwino kulalikidwa mogwilizana na cifunilo ca Mulungu. Ngakhale cizunzo kapena ngozi zacilengedwe sizingalepheletse zimenezi. Tikakukana na mavuto, kodi timadalila Atate wathu wakumwamba na kuikabe kulambila kwake patsogolo?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani