LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 March tsa. 16
  • Makambilano Acitsanzo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Makambilano Acitsanzo
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Tumitu
  • Nkhani Zofanana
  • Kampeni Yomemeza Anthu ku Cikumbutso (February 27–March 27)
  • Ulendo Woyamba
  • Ulendo Wobwelelako
  • Makambilano Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
  • Makambilano Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
  • Makambilano Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Makambilano Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 March tsa. 16

CITANI KHAMA PA ULALIKI

Makambilano Acitsanzo

Kampeni Yomemeza Anthu ku Cikumbutso (February 27–March 27)

Ciitanilo ca mwambo wokumbukila imfa ya Yesu, ca mutu wakuti ‘Mukuitanidwa.’

“Tabwela [kapena takutumilani kapenanso takulembelani] kuti tikuitanileni ku cocitika capadela ca anthu mamiliyoni ambili. Cocitika cimeneci ni mwambo wokumbukila imfa ya Yesu.” Ndiyeno patsani munthuyo [kapena tumizani pa meseji kapena pa imelo] kapepa ka ciitanilo. “Kapepa ka ciitanilo aka kaonetsa nthawi na malo kumene cocitikaci cidzacitikile kwathu kuno [kapena mmene mungalumikizile ku msonkhanowu pa intaneti]. Tikuitanilaninso ku nkhani yapadela imene idzakambidwa kumapeto kwa mlungu woti cikumbutso cicitika mlungu wotsatila.”

Akaonetsa cidwi: Onetsani [kapena tumizani pa meseji kapena pa imelo] vidiyo yakuti Kukumbukila Imfa ya Yesu.

Ulalo: N’cifukwa ciani Yesu anafa?

Ulendo Woyamba

Funso: Kodi Yesu anali ndani?

Lemba: Mat. 16:16

Ulalo: N’cifukwa ciani Yesu anafa?

PEZANI LEMBALI M’CIDA CA M’THUBOKSI YATHU:

  • Buku lakuti ‘Zimene Baibulo Ingatiphunzitse.’

    bhs 41 ¶5

Ulendo Wobwelelako

Funso: N’cifukwa ciani Yesu anafa?

Lemba: Mat. 20:28

Ulalo: Kodi tingaonetse bwanji kuti timayamikila nsembe ya dipo la Yesu?

PEZANI LEMBALI M’CIDA CA M’THUBOKSI YATHU:

  • Buku lakuti ‘Zimene Baibulo Ingatiphunzitse.’

    bhs 52 ¶2

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani