LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 May tsa. 2
  • May 3-9

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • May 3-9
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 May tsa. 2

May 3-9

NUMERI 27–29

  • Nyimbo 106 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Tengelani Citsanzo ca Yehova ca Kupanda Tsankho”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Num. 28:7, 14—Kodi nsembe zacakumwa zinali zotani? (1 Sam. 1:11; it-2 528 ¶5)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Num. 28:11-31 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Woyamba: Colinga ca Mulungu—Gen. 1:28. Nthawi iliyonse vidiyo ikaima, na imwe iimitseni na kufunsa omvetsela mafunso amene aonekela pasikilini.

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 4)

  • Nkhani: (Mph. 5) w07 4/1 17-18—Mutu: N’ciani Cimapangitsa Nsembe Kukhala Zovomelezeka kwa Yehova? (th phunzilo 16)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 82

  • Khala Bwenzi la Yehova—Uzikonda Mnzako: (Mph. 6) Kukambilana. Onetsani vidiyoyi. Ndiyeno ngati n’kotheka, funsani ana amene munawakonzekeletsa mafunso aya: N’cifukwa ciani ana a sukulu anali kumusala Priya? Kodi Sophia anamuonetsa bwanji cikondi Priya? Kodi mungawaonetse bwanji cikondi anthu a cikhalidwe cina?

  • Kodi Bwenzi Leni-leni Limakhala Lotani?: (Mph. 9) Kukambilana. Onetsani vidiyoyi ya zithunzi zojambula pamanja. Ndiyeno funsani omvetsela mafunso aya: Kodi muyenela kusankha munthu wotani kuti akhale bwenzi lanu? Kodi bwenzi labwino mungalipeze kuti? Mungacite ciani kuti mupange ubwenzi wabwino na ena?

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 35

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 41 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani