LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 May tsa. 2
  • Tengelani Citsanzo ca Yehova ca Kupanda Tsankho

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Tengelani Citsanzo ca Yehova ca Kupanda Tsankho
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • Mmene Mungakhalile na Moyo Wopambana
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Yehova Amatidalitsa Ngati Ticita Zinthu Zoonetsa Cikhulupililo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Muzilimbikitsa Ena pa Nthawi Zovuta
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Zimene Makolo Angaphunzile kwa Manowa na Mkazi Wake
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 May tsa. 2
Ana asanu aakazi a Tselofekadi akufotokoza dandaulo lawo kwa Mose pa khomo la cihema cokumanako.

Ana aakazi a Tselofekadi akupempha colowa ca atate awo

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Tengelani Citsanzo ca Yehova ca Kupanda Tsankho

Ana asanu aakazi a Tselofekadi anapempha kuti alandile colowa ca atate awo (Num. 27:1-4; w13 6/15 10 ¶14; onani cithunzi pacikuto)

Yehova anapanga cigamulo copanda tsankho (Num. 27:5-7; w13 6/15 11 ¶15)

Ifenso tiyenela kucita zinthu mopanda tsankho (Num. 27:8-11; w13 6/15 11 ¶16)

Timatengela citsanzo ca Yehova ca kupanda tsankho mwa kucita zinthu mwaulemu na okhulupilila anzathu, kuwaonetsa cikondi cokhulupilika komanso mwa kulalikila anthu a mitundu yonse.

Zithunzi: Njila zimene tingaonetsele kupanda tsankho. 1. Mabwenzi asanu a zaka komanso mitundu yosiyana akuceza na kudyela pamodzi mosangalala m’nyumba. 2. Mwamuna na mkazi wake akulalikila munthu wa mtundu wina pafupi na msasa wa anthu othaŵa kwawo.
    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani