CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Mmene Mungakhalile na Moyo Wopambana
[Onetsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la Yoswa.]
Ŵelengani na kuseŵenzetsa Mawu a Mulungu (Yos. 1:7, 8; w13 1/15 8 ¶7)
Dalilani Yehova pamene mucita cifunilo cake (Yos. 1:9; w13 1/15 11 ¶20)
DZIFUNSENI KUTI, Ni pa zocitika ziti pamene ningafune kuti Mulungu anithandize kukhala wolimba mtima?