CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Muzilimbikitsa Ena pa Nthawi Zovuta
Senakeribu anaukila ufumu wa Yuda na kuwopseza kuti awononga mzinda wa Yerusalemu (2 Mbiri 32:1; it-1 204 ¶5)
Hezekiya anacita zonse zotheka kuti ateteze Yerusalemu (2 Mbiri 32:2-5; w13 11/15 19 ¶12)
Hezekiya analimbikitsa anthu a Mulungu (2 Mbiri 32:6-8; w13 11/15 19 ¶13)
DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ningawalimbikitse bwanji abale anga pa nthawi zovuta?’