LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 September tsa. 6
  • Yehova Amatidalitsa Ngati Ticita Zinthu Zoonetsa Cikhulupililo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yehova Amatidalitsa Ngati Ticita Zinthu Zoonetsa Cikhulupililo
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • Mmene Mungakhalile na Moyo Wopambana
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Tengelani Citsanzo ca Yehova ca Kupanda Tsankho
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Muzilimbikitsa Ena pa Nthawi Zovuta
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Malangizo Othela a Yoswa kwa Aisiraeli
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 September tsa. 6
Ansembe akuponda pa madzi othamanga a mu Mtsinje wa Yorodano atanyamula likasa la pangano

Ansembe akuloŵa pa Mtsinje wa Yorodano atanyamula Likasa

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yehova Amatidalitsa Ngati Ticita Zinthu Zoonetsa Cikhulupililo

Nthawi zina, malangizo a Yehova angaoneke osathandiza malinga n’kuona kwa anthu (Yos. 3:12, 13; it-2 105; onani cithunzi pacikuto)

Amuna a paudindo ayenela kukhala citsanzo cabwino pa nkhani yotsatila malangizo. (Yos. 3:14; w13 9/1 16 ¶17)

Yehova amadalitsa anthu amene amacita zinthu mosazengeleza (Yos. 3:15-17; w13 9/1 16 ¶18)

Ansembe akuwoloka mtsinje wa Yorodano pa nthaka youma atanyamula likasa la pangano.

Timapatsa Yehova mpata woti atidalitse ngati timayesetsa kupeza njila yolalikilila, ngakhale kuti tili na thanzi lofooka kapena pali zovuta zina.

Mlongo akulalikila mzimayi pa benchi ya ku paki, ndipo wapolisi akudutsa capafupi.
    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani