September Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano, September-October 2021 September 6-12 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Funani Citetezo M’manja a Yehova “Amene Adzakhalapo Mpaka Kale-kale” UMOYO WATHU WACIKHRISTU Seŵenzetsani Buku Lakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! mu Ulaliki September 13-19 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Mmene Mungakhalile na Moyo Wopambana UMOYO WATHU WACIKHRISTU Pitilizani Kuphunzitsa Mphamvu Zanu za Kuzindikila September 20-26 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Yehova Amatidalitsa Ngati Ticita Zinthu Zoonetsa Cikhulupililo CITANI KHAMA PA ULALIKI | WONJEZELANI CIMWEMWE CANU MU ULALIKI Seŵenzetsani Zida Zofufuzila September 27–October 3 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Pewani Zinthu Zopanda Pake October 4-10 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Zimene Tingaphunzile pa Nkhani ya Agibeoni October 11-17 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Yehova Anawamenyela Nkhondo Aisiraeli CITANI KHAMA PA ULALIKI | WONJEZELANI CIMWEMWE CANU MU ULALIKI Landilani Thandizo la Anchito Anzanu October 18-24 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Tsatilani Yehova na Mtima Wonse UMOYO WATHU WACIKHRISTU Muzim’kumbukila Yehova Nthawi Zonse October 25-31 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Tetezani Coloŵa Canu Camtengo Wapatali UMOYO WATHU WACIKHRISTU Lalikilani Uthenga Wabwino Wakuti Dziko Labwino Lili Pafupi! CITANI KHAMA PA ULALIKI Makambilano Acitsanzo