LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 September tsa. 12
  • October 18-24

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • October 18-24
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 September tsa. 12

October 18-24

YOSWA 12-14

  • Nyimbo 69 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Tsatilani Yehova na Mtima Wonse”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Yos. 13:2, 5—Kodi Aisiraeli analandiladi “dziko la Agebala”? (it-1 902-903)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Yos. 12:7-24 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Yambani na makambilano acitsanzo. Kenako, pemphani mwininyumba kuti muziphunzila naye Baibo m’bulosha yakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! (th phunzilo 6)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno gaŵilani bulosha yakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! na kuyambitsa phunzilo la Baibo m’phunzilo 01. (th phunzilo 20)

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lffi phunzilo 01 mfundo 5 (th phunzilo 18)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 84

  • Zofunikila za Mpingo: (Mph. 5)

  • “Muzim’kumbukila Yehova Nthawi Zonse”: (Mph. 10) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Tumikilani Yehova na Moyo Wanu Wonse.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 60

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 22 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani