CITANI KHAMA PA ULALIKI
Makambilano Acitsanzo
Ulendo Woyamba
Funso: N’kuti kumene tingapeze malangizo othandiza pa umoyo?
Lemba: 2 Tim. 3:16, 17
Ulalo: N’cifukwa ciani muyenela kuikhulupilila Baibo?
PEZANI LEMBALI M’CIDA CA M’TUBOKSI YATHU:
Ulendo Wobwelelako
Funso: N’cifukwa ciani muyenela kuikhulupilila Baibo?
Lemba: Yobu 26:7
Ulalo: Kodi ni mafunso ena ati amene Baibo imayankha?
PEZANI LEMBALI M’CIDA CA M’TUBOKSI YATHU: