CITANI KHAMA PA ULALIKI
Makambilano Acitsanzo
ULENDO WOYAMBA
Funso: N’kuti kumene tingapeze ulangizi wothandiza pa umoyo?
Lemba: 2 Tim. 3:16, 17
Ulalo: N’cifukwa ciyani muyenela kuikhulupilila Baibo?
PEZANI LEMBA ILI M’THUBOKSI YATHU:
ULENDO WOBWELELAKO
Funso: N’cifukwa ciyani muyenela kuikhulupilila Baibo?
Lemba: Yobu 26:7
Ulalo: Kodi ni mafunso ena ati amene Baibo imayankha?
PEZANI LEMBA ILI M’THUBOKSI YATHU: