LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 January tsa. 16
  • Makambilano Acitsanzo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Makambilano Acitsanzo
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Tumitu
  • Nkhani Zofanana
  • Ulendo Woyambaa
  • Ulendo Wobwelelakob
  • Makambilano Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Makambilano Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Makambilano Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Makambilano Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 January tsa. 16

CITANI KHAMA PA ULALIKI

Makambilano Acitsanzo

Ulendo Woyambaa

Funso: Tidziŵa bwanji kuti Mulungu amasamala za ife aliyense payekha-payekha?

Lemba: Mat. 10:29-31

Ulalo: Kodi Mulungu amatithandiza bwanji kupilila mavuto amene timakumana nawo palipano?

PEZANI LEMBALI M’CIDA CA M’TUBOKSI YATHU:

  • “Nsanja ya Mlonda” Na. 3 2018.

    wp18.3 4

Ulendo Wobwelelakob

Funso: Kodi Mulungu amatithandiza bwanji kupilila mavuto amene timakumana nawo palipano?

Lemba: Yer. 29:11

Ulalo: Kodi Baibo ingatitsogolele bwanji?

PEZANI LEMBALI M’CIDA CA M’TUBOKSI YATHU:

  • Kabuku kakuti “Kondwelani Na Moyo Kwamuyaya!”

    lffi phunzilo 2 mfundo 1

a b Mungasintheko funso na ulalo kuti zigwilizane na mikhalidwe ya kwanuko

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani