CITANI KHAMA PA ULALIKI
Makambilano Acitsanzo
Ulendo Woyamba
Funso: Kodi n’zoona kuti nkhondo komanso zaciwawa zidzatha?
Lemba: Sal. 37:10, 11
Ulalo: Ni lonjezo liti la m’Baibo limene limatipatsa ciyembekezo?
PEZANI LEMBALI M’CIDA CA M’TUBOKSI YATHU:
Ulendo Wobwelelako
Funso: Ni lonjezo liti la m’Baibo limene limatipatsa ciyembekezo?
Lemba: Chiv. 21:3, 4
Ulalo: Kodi n’ciyani cingatithandize kuimvetsetsa Baibo?
PEZANI LEMBALI M’CIDA CA M’TUBOKSI YATHU: