LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 January tsa. 8
  • January 31–February 6

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • January 31–February 6
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 January tsa. 8

January 31–February 6

RUTE 3-4

  • Nyimbo 39 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Pangani Mbili Yabwino Ndipo Isungeni”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Rute 4:6—Kodi munthu wowombola ‘akanawononga’ bwanji colowa cake powombola mkazi? (w05 3/1 29 ¶3)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Rute 4:7-22 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • “Wonjezelani Cimwemwe Canu mu Ulaliki—Thandizani Maphunzilo Anu a Baibo Kumapezeka pa Misonkhano”: (Mph. 10) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Thandizani Maphunzilo Anu a Baibo Kumapezeka pa Misonkhano.

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lffi phunzilo 03 mfundo 4 (th phunzilo 8)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 24

  • Zofunikila za Mpingo: (Mph. 15)

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 75

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 13 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani