LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 January tsa. 12
  • February 14-20

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • February 14-20
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 January tsa. 12

February 14-20

1 SAMUELI 3-5

  • Nyimbo 1 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yehova Ni Mulungu Woganizila Ena”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 1 Sam. 3:3—Tidziŵa bwanji kuti Samueli sanali kugona m’Malo Oyela Koposa? (w05 3/15 21 ¶6)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 1 Sam. 3:1-18 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Yambani na makambilano acitsanzo. Pemphani mwininyumba kuti muziphunzila naye Baibo m’kabuku kakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya. (th phunzilo 11)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo. Gaŵilani kabuku kakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! na kuyambitsa phunzilo la Baibo m’phunzilo 01. (th phunzilo 15)

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lffi phunzilo 03 mfundo 6 (th phunzilo 14)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 30

  • “Zimene Tingaphunzile kwa Samueli”: (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Zimene Tingaphunzile Kwa Iwo—Samueli.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 77

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 64 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani