LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 May tsa. 6
  • Khalanibe na Mantha Oyenela Oopa Kukhumudwitsa Yehova

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Khalanibe na Mantha Oyenela Oopa Kukhumudwitsa Yehova
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Zofanana
  • Phunzitsani Ana Anu Kukonda Yehova
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Davide Anaonetsa Cikondi Cosasintha
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Zimene Makolo Angaphunzile kwa Manowa na Mkazi Wake
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Na Thandizo la Yehova, Mungakwanitse Kucita Utumiki Wovuta
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 May tsa. 6
Uza watambasula dzanja lake kucilikiza likasa la pangano kuti lisagwe.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Khalanibe na Mantha Oyenela Oopa Kukhumudwitsa Yehova

Kukhala na zolinga zabwino si cifukwa cophwanyila malamulo a Yehova (2 Sam. 6:3-5; w05 5/15 17 ¶8)

Uza anaphwanya lamulo la Mulungu (2 Sam. 6:6; w05 2/1 27 ¶20)

Yehova analanga Uza cifukwa cocita cinthu cosalemekeza Mulungu (2 Sam. 6:7; w05 2/1 27 ¶21)

DZIFUNSENI KUTI, ‘Pa umoyo wanga, ningaonetse bwanji kuti nimaopa kukhumudwitsa Yehova?’—Miy. 3:7

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani