LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 May tsa. 9
  • Davide Anaonetsa Cikondi Cosasintha

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Davide Anaonetsa Cikondi Cosasintha
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Zofanana
  • Khalanibe na Mantha Oyenela Oopa Kukhumudwitsa Yehova
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Mafunso Ocokela kwa Oŵelenga
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2022
  • Khalani Wokhulupilika kwa Yehova
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2016
  • Tengelani Citsanzo ca Atumiki Okhulupilika a Yehova
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2016
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 May tsa. 9

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Davide Anaonetsa Cikondi Cosasintha

Davide anafuna-funa munthu amene akanamuonetsa cikondi cosasintha (2 Sam. 9:1; w06 6/15 14 ¶6)

Davide anacitapo kanthu mwamsanga kuti athandize Mefiboseti (1 Sam. 20:15, 42; 2 Sam. 9:5-7; w05 5/15 17 ¶12)

Davide anapatsa Ziba udindo wosamalila coloŵa ca Mefiboseti (2 Sam. 9:9, 10; w02 2/15 14 ¶10)

Mlongo wacikulile wakumbatila mlongo wacitsikana, ndipo akumutonthoza.

Davide sanaiŵale lonjezo lake kwa Yonatani. Tiyenela kuonetsa cikondi cosasintha kwa okhulupilila anzathu.—Sal. 41:1, 2; Miy. 19:17.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani