LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 May tsa. 10
  • Musalole Zilakolako Zoipa Kukulamulilani

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Musalole Zilakolako Zoipa Kukulamulilani
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Zofanana
  • Zimene Zimabweletsa Macimo na Imfa
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
  • “Sandulikani mwa Kusintha Maganizo Anu”
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2023
  • Kodi Mukumbukila?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2019
  • Kodi Mukukumbukila?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2021
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 May tsa. 10
Davide ali pa denga la nyumba yake, ndipo akuyang’ana Bati-seba.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Musalole Zilakolako Zoipa Kukulamulilani

Davide analola cilakolako coipa kukula mu mtima mwake (2 Sam. 11:2-4; w21.06 17 ¶10)

Davide anaseŵenzetsa mphamvu zake molakwika pofuna kubisa chimo lake (2 Sam. 11:5, 14, 15; w19.09 17 ¶15)

Davide anakumana na mavuto aakulu cifukwa ca chimo lake (2 Sam. 12:9-12; w18.06 17 ¶7)

Kuti tipewe kuyang’ana kapena kuganizila zinthu zoipa, tifunika kudziletsa. (Agal. 5:16, 22, 23) Yehova angatithandize kuti tisamalole zilakolako zoipa kuzika mizu mu mtima mwathu.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi niyenela kulamulila maganizo anga makamaka pa mbali ziti?’

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani