LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 July tsa. 9
  • Dzipelekeni Kuthandiza pa Nchito Zomanga za Gulu

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Dzipelekeni Kuthandiza pa Nchito Zomanga za Gulu
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Zofanana
  • Kodi Mungapeleke Nthawi na Mphamvu Zanu?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
  • Muziseŵenza na Yehova Tsiku Lililonse
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2018
  • Njila Zowonjezela Utumiki Wanu
    Gulu Lokhazikitsidwa Kucita Cifunilo ca Yehova
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 July tsa. 9

UMOYO WATHU WACIKHRISTU | DZIIKILENI ZOLINGA ZA CAKA CA UTUMIKI CATSOPANO

Dzipelekeni Kuthandiza pa Nchito Zomanga za Gulu

Kugwila nchito za mamangidwe za m’gulu lathu ni mbali ya utumiki wopatulika. (Eks. 36:1) Kodi nthawi na nthawi mungadzipeleke kuthandiza pa nchito zomanga za kufupi na kwanuko? Ngati n’conco, sainani fomu ya DC-50. Kapena mungadzipeleke kukathandiza pa nchito zomanga za kutali na kwanu kwa milungu kapena miyezi? Ngati n’conco, sainani fomu ya A-19. Sizilila kuti munthu akhale na luso la zomangamanga kuti athandize pa nchito za mamangidwe za m’gulu lathu.—Neh. 2:1, 4, 5.

ONELELANI VIDIYO YAKUTI LOŴANI PA KHOMO LA ZOCITA ZAMBILI M’CIKHULUPILILO—DZIPELEKENI KUTHANDIZA PA NCHITO ZOMANGA ZA GULU, KENAKO YANKHANI MAFUNSO AWA:

  • Cithunzi coonetsa zocitika za m’vidiyo yakuti “Loŵani pa Khomo la Zocita Zambili M’cikhulupililo—Dzipelekeni Kuthandiza pa Nchito Zomanga za Gulu.” Sarah wavala cisoti colimba, ndipo akuoneka wosangalala pa malo ogwilila nchito yomanga.

    Kodi Sarah anali kudela nkhawa za ciyani? Nanga cinam’thandiza n’ciyani?

Ngati colinga canu ni kuthandiza pa nchito za mamangidwe za m’gulu, kambani na akulu a mumpingo wanu, ndipo adzakuthandizani kufunsila utumikiwu.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani