LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 July tsa. 12
  • August 22-28

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • August 22-28
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 July tsa. 12

August 22-28

1 MAFUMU 7

  • Nyimbo 7 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Zimene Tingaphunzilepo pa Zipilala Ziŵili”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 1 Maf. 7:23—Kodi “thanki yamkuwa” yaikulu imene inamangidwa pa kacisi itiphunzitsa ciyani? (it-1 263)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 1 Maf. 7:1-12 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Mukayamba kukambilana, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 6)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Ndipo m’gaŵileni kabuku kakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! na kumuonetsa mmene phunzilo la Baibo limacitikila. (th phunzilo 3)

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 06 mfundo 6, na mbali yakuti Anthu Ena Amakamba Kuti (th phunzilo 8)

UMOYO WATHU WACIKHRSITU

  • Nyimbo 72

  • Zofunikila za Mpingo: (Mph. 5)

  • “Kampeni Yapadela Yoyambitsa Maphunzilo a Baibo mu September”: (Mph. 10) Nkhani yokambilana yokambidwa na woyang’anila utumiki. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Woyamba: Phunzilo la Baibo—Sal. 37:29. Fotokozani makonzedwe amene mpingo wapanga okhudza kampeni imeneyi.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 17

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 13 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani