LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 January tsa. 3
  • January 9-15

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • January 9-15
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 January tsa. 3

January 9-15

2 MAFUMU 24-25

  • Nyimbo 60 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Khalanibe Maso”:(Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 2 Maf. 24:3, 4—Kodi mavesi awa atiphunzitsa ciyani za Yehova? (w05 8/1 12 ¶1)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulila iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 2 Maf. 24:1-17 (th phunzilo 11)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Wobwelelako: Pemphelo—1 Yoh. 5:14. Nthawi zonse vidiyo ikaima, inunso iimitseni na kufunsa omvela mafunso amene aonekela.

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. (th phunzilo 15)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 5) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo, ndipo yambitsani phunzilo la Baibo m’phunzilo 01 la bulosha yakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! (th phunzilo 19)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 143

  • Zofunikila za Mpingo: (Mph. 15)

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff kubweleza cigawo 2

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 54 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani