LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 January tsa. 6
  • Kodi Mapemphelo Anga Amavumbula Ciyani za Ine?

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kodi Mapemphelo Anga Amavumbula Ciyani za Ine?
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • Yandikilani kwa Mulungu Kupitila M’pemphelo
    Zimene Baibo Imaphunzitsa M’ceni-ceni
  • Mawu Oyamba
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2021
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 January tsa. 6

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kodi Mapemphelo Anga Amavumbula Ciyani za Ine?

Yabezi anali munthu wolemekezeka (1 Mbiri 4:9)

Pemphelo lake linaonetsa kuti anali kukonda kulambila koona (1 Mbiri 4:10a; w10 10/1 23 ¶3-7)

Yehova anayankha pemphelo la Yabezi (1 Mbiri 4:10b)

Mlongo wacikulile akupemphela mokhudzika mtima. Pa mendo pake pali Baibo na mndandanda wa pa jw.org wa maina a abale amene ali m’ndende.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi mapemphelo anga amavumbula ciyani za ine?’—Mat. 6:9, 10.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani