LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 January tsa. 6
  • January 23-29

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • January 23-29
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 January tsa. 6

January 23-29

1 MBIRI 4-6

  • Nyimbo 42 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kodi Mapemphelo Anga Amavumbula Ciyani za Ine?”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 1 Mbiri 5:10—Kodi kugonjetsedwa kwa Ahagara kungatilimbikitse bwanji pamene tikukumana na mavuto aakulu mu umoyo wathu? (w05 10/1 9 ¶7)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulila iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 1 Mbiri 6:61-81 (th phunzilo 2)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Mukayamba, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 3)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitanzo. Chulani na kukambilanako vidiyo yakuti N’cifukwa Ciani Muyenela Kuphunzila Baibulo? (Koma musaitambitse.) (th phunzilo 14)

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 8 cidule cake, kubweleza, komanso colinga (th phunzilo 9)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 127

  • “Konzekelani Palipano Musanadwale Mwadzidzidzi Kapena Kukumana na Ngozi”: (Mph. 15) Kukambilana na kutamba vidiyo. Nkhaniyi ipatsidwe kwa mkulu. Patsani omvela nthawi kuti akambepo zimene aphunzila mu vidiyo.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 35

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 88 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani