January Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano, January-February 2023 January 2-8 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU N’cifukwa Ciyani Tiyenela Kukhala Odzicepetsa? January 9-15 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Khalanibe Maso January 16-22 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Baibo—Buku Limene Limakamba Zenizeni Osati Nthano UMOYO WATHU WACIKHRISTU Limbitsani Cikhulupililo Canu pa Mawu a Mulungu January 23-29 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Kodi Mapemphelo Anga Amavumbula Ciyani za Ine? UMOYO WATHU WACIKHRISTU Konzekelani Palipano Musanadwale Mwadzidzidzi Kapena Kukumana na Ngozi January 30–February 5 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Na Thandizo la Yehova, Mungakwanitse Kucita Utumiki Wovuta UMOYO WATHU WACIKHRISTU Yehova Amatithandiza Kupilila Mayeso February 6-12 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Kulitsani Cikhumbo Canu Cofuna Kucita Cifunilo ca Mulungu UMOYO WATHU WACIKHRISTU Fufuzani Kuti Mudziŵe Maganizo a Mulungu UMOYO WATHU WACIKHRISTU Dziikileni Zolinga za pa Nyengo ya Cikumbutso February 13-19 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Kutsatila Malangizo Kumacititsa Kuti Zinthu Zitiyendele Bwino February 20-26 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Khalanibe Acimwemwe Ngakhale Pamene Mwakumana na Zolefula February 27–March 5 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Thandizani Acinyamata Kuti Apambane UMOYO WATHU WACIKHRISTU Seŵenzetsani Mfundo za m’Baibo Pothandiza Ana Anu Kuti Apambane CITANI KHAMA PA ULALIKI Makambilano Acitsanzo