LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 May tsa. 10
  • June 5-11

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • June 5-11
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 May tsa. 10

June 5-11

2 MBIRI 30–31

  • Nyimbo 87 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kusonkhana Pamodzi Kumatipindulila”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 2 Mbiri 30:20—Tiphunzilapo ciyani tikaganizila mmene Yehova anayankhila pemphelo la Hezekiya? (w18.09 6 ¶14-15)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 2 Mbiri 31:11-21 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 2) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. (th phunzilo 20)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph.5) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’gaŵileni bulosha yakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! na kuyambitsa phunzilo la Baibo m’phunzilo 01. (th phunzilo 18)

  • Nkhani: (Mph. 5) w19.01 11-12 ¶13-18—Mutu: Tamandani Yehova mwa Kupeleka Ndemanga pa Misonkhano. (th phunzilo 16)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 74

  • Khala Bwenzi la Yehova—Konzekela Yankho Lako: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyoyi. Ndiyeno ngati n’zotheka, funsani acicepele m’gulu mafunso awa: Kodi mungakonzekele bwanji kuti mukapelekepo ndemanga pa msonkhano? N’cifukwa ciyani tingakhalebe acimwemwe ngakhale kuti sanatipatseko mwayi wopelekapo ndemanga?

  • Zimene Gulu Lakwanitsa Kucita: (Mph. 10) Onetsani vidiyo ya Zimene Gulu Lakwanitsa kucita ya June.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff mafunso obweleza a cigawo 3

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 115 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani