LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 May tsa. 12
  • Kodi Mumapindula Nawo Mofikapo Mawu a Mulungu?

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kodi Mumapindula Nawo Mofikapo Mawu a Mulungu?
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • Yehova Amadalitsa Anthu Ocita Zinthu Molimba Mtima
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Yosiya Anali ndi Anzake Abwino
    Phunzitsani Ana Anu
  • “Khulupililani Yehova Mulungu Wanu”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Kutumikila Yehova Sikovuta
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 May tsa. 12
Mfumu Yosiya akung’amba malaya ake cifukwa ca cisoni.

Yosiya akung’amba covala cake pamene akumva buku la Cilamulo ca Yehova likuŵelengedwa mokweza

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kodi Mumapindula Nawo Mofikapo Mawu a Mulungu?

Yosiya anamvetsela Mawu a Mulungu mosamala (2 Mbiri 34:18, 19; onani cithunzi ca pacikuto)

Iye anayesetsa kumvetsa tanthauzo la zimene anali kumvetsela (2 Mbiri 34:21; it-1 1157 ¶4)

Yosiya anacitapo kanthu pa zimene anaphunzila (2 Mbiri 34:33; w09 6/15 10 ¶20)

Pambuyo poŵelenga Baibo, m’bale akutaya ma CD a maseŵelo aciwawa a pa vidiyo.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi nimacitapo kanthu mwamsanga pa zimene nimaphunzila za Yehova m’Mawu ake Baibo?’

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani