LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 September tsa. 4
  • September 18-24

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • September 18-24
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 September tsa. 4

September 18-24

ESITERE 6-8

  • Nyimbo 115 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Citsanzo Cimene Tingatengele pa Nkhani ya Kulankhulana Bwino”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Esitere 7:4—Kodi kuwonongedwa kwa Ayuda ‘kukanawonongetsa bwanji zinthu zambili za Mfumu’? (w06 3/1 11 ¶1)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Esitere 8:​9-17 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Mukayamba, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki, koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 3)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Muitanileni ku misonkhano. Kenako, chulani na kukambilanako vidiyo yakuti N’ciani Cimacitika ku Nyumba ya Ufumu? (Koma musaitambitse.) (th phunzilo 12)

  • Nkhani: (Mph. 5) w22.01 10-11 ¶8-10—Mutu: Muziphunzitsa Mogwila Mtima Monga Yakobo—Uthenga Wanu Uzikhala Wosavuta Kumva. (th phunzilo 17)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 148

  • “Muzidalila Yehova Pamene Mukuvutitsidwa”: (Mph. 15) Kukambilana na kutamba vidiyo.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 58

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 124 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani