LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 November tsa. 2
  • November 6-12

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • November 6-12
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 November tsa. 2

November 6-12

YOBU 13-14

  • Nyimbo 151 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Munthu Akafa, Kodi Angakhalenso Ndi Moyo?”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Yobu 13:12—N’cifukwa ciyani Yobu anayelekezela zokamba za anzake acinyengo na “miyambi yopanda pake ngati phulusa”? (it-1 191)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Yobu 13:​1-28 (th phunzilo 12)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (Mph. 5) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Ulendo Woyamba: Baibo—2 Tim. 3:​16, 17. Nthawi zonse vidiyo ikaima, inunso iimitseni na kufunsa omvela mafunso amene aonekela.

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Kenako m’gaŵileni bulosha yakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! (th phunzilo 2)

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff mafunso obweleza a cigawo 1, mafunso 1-5 (th phunzilo 19)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 127

  • “‘Muziika Kenakake Pambali’”: (Mph. 15) Kukambilana na kutamba vidiyo. Ikambidwe na mkulu. Yamikilani mpingo cifukwa copeleka ndalama zimene zimathandiza kupititsa patsogolo zinthu za Ufumu.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) bt mutu 1 ¶16-21

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 76 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani