November Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano, November-December 2023 November 6-12 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Munthu Akafa, Kodi Angakhalenso Ndi Moyo? UMOYO WATHU WACIKHRISTU ‘Muziika Kenakake Pambali’ November 13-19 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Pewani Kutengela Elifazi Popeleka Citonthozo November 20-26 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Musawasiye Konse Alambili Anzanu UMOYO WATHU WACIKHRISTU Makonzedwe Olimbikitsa Atumiki a pa Beteli November 27–December 3 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Cuma Sicimapangitsa Munthu Kukhala Wolungama UMOYO WATHU WACIKHRISTU Mukhale Okhutila Ndi Zimene Muli Nazo December 4-10 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU ‘Kodi Munthu Angakhale Waphindu kwa Mulungu?’ UMOYO WATHU WACIKHRISTU Makolo—Phunzitsani Ana Anu Kukondweletsa Mulungu December 11-17 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Tingakhale na Mtima Wosagaŵikana Ngakhale Ndife Opanda Ungwilo UMOYO WATHU WACIKHRISTU Kugwilizana Pakati pa Kusunga Umphumphu na Maganizo Athu December 18-24 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Kodi Mbili Yanu ili Ngati ya Yobu? UMOYO WATHU WACIKHRISTU Zimene Ningacite Kuti Niteteze Mbili Yabwino ya Gulu Lathu December 25-31 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Zimene Zinathandiza Yobu Kukhalabe Woyela UMOYO WATHU WACIKHRISTU Cifukwa Cake Kuonelela Zamalisece N’koipa CITANI KHAMA PA ULALIKI Makambilano Acitsanzo