LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 November tsa. 8
  • December 4-10

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • December 4-10
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 November tsa. 8

December 4-10

YOBU 22-24

  • Nyimbo 49 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “‘Kodi Munthu Angakhale Waphindu kwa Mulungu?’”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Yobu 23:13—Kodi citsanzo ca Yehova cingatithandize bwanji kukwanilitsa zolinga zathu zauzimu? (w04 7/15 21-22)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Yobu 22:​1-22 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Muuzeni za webusaiti yathu, na kumusiyila kakhadi koloŵela pa jw.org. (th phunzilo 11)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Chulani na kukambilanako vidiyo yakuti N’cifukwa Ciani Muyenela Kuphunzila Baibulo? (Koma musaitambitse) (th phunzilo 2)

  • Nkhani: (Mph. 5) w21.05 18-19 ¶17-20—Mutu: Kukhala na Maganizo Oyenela Kumapangitsa Yehova Kupitiliza Kutiseŵenzetsa. (th phunzilo 20)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 134

  • “Makolo—Phunzitsani Ana Anu Kukondweletsa Mulungu”: (Mph. 10) Kukambilana na kutamba vidiyo.

  • Zofunikila za Mpingo: (Mph. 5)

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) bt mutu 3 ¶1-3, mabokosi pa mas. 23, 24, 25, 26, na 27

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 25 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani