LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 25
  • Cuma Capadela

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Cuma Capadela
  • ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Cuma Capadela
    Imbilani Yehova—Nyimbo Zatsopano
  • Ndise Mboni za Yehova!
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Tamandani Yehova Chifukwa cha Ufumu Wake
    Imbirani Yehova
  • Tamandani Ya Kaamba ka Mwana Wake Wodzozedwayo
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
Onaninso Zina
‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
sjj nyimbo 25

NYIMBO 25

Cuma Capadela

Yopulinta

(1 Petulo 2:9)

  1. 1. Odzozedwa na mzimu,

    Atamanda Yehova.

    Iye anaŵasankha,

    Ndipo aŵakonda.

    (KOLASI)

    Odzozedwa anu,

    Amakutamandani.

    Amakukondani,

    Amalengeza dzina lanu.

  2. 2. Monga mtundu woyela,

    Aphunzitsa co’nadi.

    M’lungu aŵaitana

    Kucoka mu mdima.

    (KOLASI)

    Odzozedwa anu,

    Amakutamandani.

    Amakukondani,

    Amalengeza dzina lanu.

  3. 3. Ni okhulupilika,

    Amaitana ena,

    Kuti aloŵe m’khola

    la a nkhosa zina.

    (KOLASI)

    Odzozedwa anu,

    Amakutamandani.

    Amakukondani,

    Amalengeza dzina lanu.

(Onaninso Yes. 43: 20b, 21; Mal. 3:17; Akol. 1:13.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani