Nyimbo 147
Cuma Capadela
Yopulinta
(1 Petulo 2:9)
Odzozedwa na mzimu,
Atamanda Yehova.
Iye anaŵasankha,
Ndipo aŵakonda.
(KOLASI)
Odzozedwa anu,
Amakutamandani.
Amakukondani,
Amalengeza dzina lanu.
Monga mtundu woyela,
Aphunzitsa co’nadi.
M’lungu aŵaitana
Kucoka ku mdima.
(KOLASI)
Odzozedwa anu,
Amakutamandani.
Amakukondani,
Amalengeza dzina lanu.
Ni okhulupilika,
Amaitana ena,
Kuti aloŵe m’khola
La a nkhosa zina.
(KOLASI)
Odzozedwa anu,
Amakutamandani.
Amakukondani,
Amalengeza dzina lanu.
(Onaninso Yes. 43:20b, 21; Mal. 3:17; Akol. 1:13.)