LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • snnw nyimbo 138 tsa. 3
  • Dzina Lanu Ndimwe Yehova

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Dzina Lanu Ndimwe Yehova
  • Imbilani Yehova—Nyimbo Zatsopano
  • Nkhani Zofanana
  • Dzina Lanu Ndimwe Yehova
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Aphunzitseni Kucilimika
    Imbilani Yehova—Nyimbo Zatsopano
  • Umoyo wa Mpainiya
    Imbilani Yehova—Nyimbo Zatsopano
  • Khalani ndi Moyo Wopambana
    Imbirani Yehova
Onaninso Zina
Imbilani Yehova—Nyimbo Zatsopano
snnw nyimbo 138 tsa. 3

Nyimbo 138

Dzina Lanu Ndimwe Yehova

Yopulinta

(Salimo 83:18)

  1. Mulungu woona,

    Wacilengedwe conse

    Imwe ndimwe Yehova

    Ku mibadwo yonse.

    Ndise onyadila

    Kukhala mpingo wanu.

    Tilengeza za imwe

    Ku mitundu yonse.

    (KOLASI)

    Yehova, Yehova,

    Ndimwe M’lungu mwekha.

    Kumwambako ndi padziko

    Kulibenso wina.

    Mulungu wamphamvu zonse

    Titamanda imwe.

    Yehova, Yehova,

    M’lungu wathu ndimwe mwekha.

  2. Ise timakhala

    Ciliconse mufuna,

    Mwa cifunilo canu

    Sitimalephela.

    Mwatipatsa dzina;

    tichedwa mboni zanu.

    Uyu ni mwai wathu

    Ndise anthu anu.

    (KOLASI)

    Yehova, Yehova,

    Ndimwe M’lungu mwekha.

    Kumwambako ndi padziko

    Kulibenso wina.

    Mulungu wamphamvu zonse

    Titamanda imwe.

    Yehova, Yehova,

    M’lungu wathu ndimwe mwekha.

(Onaninso 2 Mbiri 6:14; Sal. 72:19; Yes. 42:8.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani