LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 November tsa. 12
  • December 18-24

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • December 18-24
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 November tsa. 12

December 18-24

YOBU 28-29

  • Nyimbo 39 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kodi Mbili Yanu Ili Ngati ya Yobu?”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Yobu 29:24—Kodi tiphunzilapo ciyani pa citsanzo ca Yobu? (g00 7/8 11 ¶3)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Yobu 28:​1-28 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’gaŵileni bulosha yakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! (th phunzilo 3)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’gaŵileni bulosha yakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya!, na kukambilana naye mwacidule mbali yakuti “Zimene Muyenela Kucita Kuti Mupindule Kwambili na Maphunzilo a Baibo Amenewa.” (th phunzilo 17)

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 13, mawu oyamba pa cigawo cakuti Kumbani Mozamilapo na mfundo 4 (th phunzilo 6)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 121

  • “Zimene Ningacite Kuti Niteteze Mbili Yabwino ya Gulu Lathu”: (Mph. 15) Kukambilana na kutamba vidiyo.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) bt mutu 3 ¶12-18

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 50 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani