November 13-19
YOBU 15-17
Nyimbo 90 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Pewani Kutengela Elifazi Popeleka Citonthozo”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
Yobu 16:22—Kodi zimene Yobu anakamba zionetsa kuti sanali kukhulupilila kuti akufa adzauka? (w06 3/15 14 ¶11)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Yobu 17:1-16 (th phunzilo 12)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako: (Mph. 5) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Ulendo Wobwelelako: Baibo—Yobu 26:7. Nthawi zonse vidiyo ikaima, inunso iimitseni na kufunsa omvela mafunso amene aonekela.
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Muuzeni za pulogilamu yathu yophunzitsa Baibo na kumusiyila kakhadi kopemphela phunzilo la Baibo. (th phunzilo 11)
Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff mafunso obweleza a cigawo 1, mafunso 6-10 (th phunzilo 8)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Zofunikila za Mpingo: (Mph. 15)
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) bt mutu 2 ¶1-7, komanso mawu oyamba a cigawo 1
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 118 na Pemphelo