Zina Zimene Zilipo Pa Jw.Org
MFUNDO ZOTHANDIZA MABANJA
Mmene Mungathandizile Ana Anu Akamalephela Zinazake
Kulakwa si nkhani yacilendo. Muzithandiza ana anu kuti asamabise zimene zacitika, komanso kuti asamadzione kuti ni olephela.
Pitani pa jw.org ku Chichewa, pa mbali yakuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ANTHU OKWATIRANA KOMANSO MABANJA > KULELA ANA.
ZOCHITIKA PA MOYO WA A MBONI ZA YEHOVA
N’cifukwa ciani acinyamata 5 anaima kuti athandize munthu wina ngakhale kuti kunali kugwa sinoo komanso kunali kuzizila kwambili?
Pitani pa jw.org ku Chichewa, pa mbali yakuti ZOKHUDZA IFEYO > ZOCHITIKA PA MOYO WA A MBONI ZA YEHOVA > KUUZA ENA CHOONADI CHA M’BAIBULO.