LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • w20 July masa. 1-32
  • Yophunzila

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yophunzila
  • Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2020
Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2020
w20 July masa. 1-32
Nsanja ya Mlonda Yophunzila, July 2020.

Yophunzila

JULY 2020

NKHANI ZOPHUNZILA: AUGUST 31–SEPTEMBER 27, 2020

© 2020 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania

Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika pa dziko lonse lapansi. Nchito imeneyi timaiyendetsa na zopeleka zaufulu. Kuti mupange copeleka, pitani pa copeleka.jw.org.

Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, ena mwa masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.

CITHUNZI CA PA CIKUTO:

Davide anali kuoneka monga wopanda mphamvu ndiponso anali wacicepele, koma sanaope kumenyana na Goliyati. Iye anadalila Yehova cifukwa anali kudziŵa kuti adzamupatsa mphamvu zomuthandiza kugonjetsa Goliyati, ndipo anamuthandizadi (Onani nkhani yophunzila 29, ndime 11)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani