Zina Zimene Zilipo Pa JW.ORG
BAIBULO LIMASINTHA ANTHU
“Ndinasiya Kudziona Ngati Wosafunika”
Ŵelengani nkhaniyi kuti muone zimene a Israel Martínez anacita kuti athane na vuto lalikulu limene anali nalo lodziona ngati wosafunika.
Pitani pa jw.org ku Chichewa, pa mbali yakuti ZOKHUDZA IFEYO > ZOCHITIKA PA MOYO WA A MBONI ZA YEHOVA > BAIBULO LIMASINTHA ANTHU.
ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA
Kodi Ndingatani Kuti Ndisamangoganizira Zinthu Zolakwika?
Malangizo otsatilawa angakuthandizeni kupewa kumangoganizila zolakwika.
Pitani pa jw.org ku Chichewa, pa mbali yakuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ACHINYAMATA > ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA.