Yophunzila
AUGUST 2020
NKHANI ZOPHUNZILA: SEPTEMBER 28–NOVEMBER 1, 2020
© 2020 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika pa dziko lonse lapansi. Nchito imeneyi timaiyendetsa na zopeleka zaufulu. Kuti mupange copeleka, pitani pa copeleka.jw.org.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, ena mwa masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.
CITHUNZI CA PA CIKUTO:
Yesu ali kumwamba. Pafupi na iye paimilila ena mwa olamulila anzake. Iwo pamodzi na Yesu akuyang’ana angelo miyanda-miyanda. Angelo ena akupita ku dziko lapansi kukacita nchito zawo. Onse amene ali pa cithunzici, Yehova anawagaŵila zocita (Onani nkhani yophunzila 32, ndime 5)