Zina Zimene Zilipo Pa JW.ORG
MFUNDO ZOTHANDIZA MABANJA
Kodi Mungatani Kuti Zipangizo Zamakono Zisamakusokonezeni?
Zipangizo zamakono zikhoza kulimbitsa kapena kusokoneza banja lanu. Kodi zimenezi zingachitike bwanji?
Pitani pa jw.org ku Chichewa, pa mbali yakuti, LAIBULALE > NKHANI ZOSIYANASIYANA > MFUNDO ZOTHANDIZA MABANJA.
FROM OUR ARCHIVES
Akulu-akulu a boma ayamikila kwambili Mboni za Yehova pa nchito imene amacita yophunzitsa anthu kulemba na kuŵelenga.
Pitani pa jw.org ku Cizungu, pa mbali yakuti, LIBRARY > ARTICLE SERIES > FROM OUR ARCHIVES.